16 Wakhaliranji pakati pa makola,Kumvera kulira kwa zoweta?Ku timitsinje ta Rubeni kunali zotsimikiza mtima zazikuru.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 5
Onani Oweruza 5:16 nkhani