Oweruza 5:26 BL92

26 Dzanja lace analitambasulira kuciciri,Ndi dzanja lace lamanja ku nyundo ya anchito,Nakhomera Sisera, nakantha mutu wace,Inde, anaphwanya napyoza m'litsipa mwace.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 5

Onani Oweruza 5:26 nkhani