31 Adani anu onse, Yehova, atayike momwemo.Koma iwo akukonda Inu akhale ngati dzuwa loturuka mu mphamvu yace.Ndipo dziko linapumula zaka makumi anai.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 5
Onani Oweruza 5:31 nkhani