15 Ndipo anati kwa iye, Ha! Mbuye, ndidzapulumutsa Israyeli ndi ciani? Taonani, banja langa liri loluluka m'Manase, ndipo ine ndine wamng'ono m'nyumba ya atate wanga.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 6
Onani Oweruza 6:15 nkhani