Oweruza 6:2 BL92

2 Pamene dzanja la Midyani linalaka Israyeli, ana a Israyeli anadzikonzera ming'ang'ala ya m'mapiri, ndi mapanga, ndi malinga cifukwa ca Midyani.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 6

Onani Oweruza 6:2 nkhani