Oweruza 6:22 BL92

22 Pamenepo Gideoni anaona kuti ndiye mthenga wa Yehova, nati Gideoni, Tsoka ine, Yehova Mulungu! popeza ndaona mthenga wa Yehova maso ndi maso.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 6

Onani Oweruza 6:22 nkhani