Oweruza 6:25 BL92

25 Ndipo kunali, usiku womwe uja Yehova ananena naye, Tenga ng'ombe ya atate wako, ndiyo ng'ombe yaciwiri ya zaka zisanu ndi ziwiri, nugamule guwa la nsembe la Baala ndilo la atate wako, nulikhe cifanizo ciri pomwepo;

Werengani mutu wathunthu Oweruza 6

Onani Oweruza 6:25 nkhani