Oweruza 6:30 BL92

30 Pamenepo amuna a ku mudziwo anati kwa Yoasi, Umturutse mwana wako kuti afe; pakuti anagamula guwa la nsembe la Baala, pakutinso analikha cifanizo cinali pomwepo.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 6

Onani Oweruza 6:30 nkhani