Oweruza 6:37 BL92

37 taonani, ndidzaika cikopa ca ubweya popunthira tirigu; pakakhala mame pacikopa pokha, ndi panthaka ponse pouma, pamenepo ndidzadziwa kuti mudzapulumutsa Israyeli ndi dzanja langa monga mwanena.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 6

Onani Oweruza 6:37 nkhani