Oweruza 6:8 BL92

8 Yehova anatuma munthu mneneri kwa ana a Israyeli, nanena nao, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Ine ndinakukwezani kucokera m'Aigupto, ndi kukuturutsani m'nyumba ya ukapolo;

Werengani mutu wathunthu Oweruza 6

Onani Oweruza 6:8 nkhani