Oweruza 7:12 BL92

12 Ndipo Amidyani ndi Aamaleki ndi ana onse a kum'mawa ali gonere m'cigwa, kucuruka kwao ngati dzombe; ndi ngamila zao zosawerengeka, kucuruka kwao ngati mcenga wa m'mphepete mwa nyanja.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 7

Onani Oweruza 7:12 nkhani