Oweruza 7:5 BL92

5 Ndipo anatsikira nao anthu kumadzi; ndipo Yehova anati kwa Gideoni, Ali yense akapiza madzi pa lilime lace, monga akhatira garu, ameneyo amuike pa yekha; momwemo ali yense agwada pakumwa.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 7

Onani Oweruza 7:5 nkhani