Oweruza 8:11 BL92

11 Ndipo Gideoni anakwerera njira ya iwo okhala m'mahema kum'mawa kwa Noba, ndi Yogibea, nakantha khamulo popeza khamulo linakhala lokhazikika mtima.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 8

Onani Oweruza 8:11 nkhani