Oweruza 9:16 BL92

16 Ndipo tsopano, ngati mwacita moona ndi mwangwiro pakulonga Abimeleki ufumu, ngatinso mwamcitira cokoma Yerubaala ndi nyumba yace, ndi kumcitira monga anayenera manja ace;

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:16 nkhani