Oweruza 9:3 BL92

3 Pamenepo abale a amace anamnenera mau awa onse m'makutu a eni ace onse a Sekemu; ndi mitima yao inalunjika kutsata Abimeleki; pakuti anati, Ndiye mbale wathu.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:3 nkhani