Oweruza 9:33 BL92

33 ndipo kukhale kuti m'mawa, pakuturuka dzuwa, muuke mamawa mugwere mudziwo; ndipo taonani, akakuturukirani iye ndi anthu ali naye, uzimcitira monga lidziwa dzanja lako.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:33 nkhani