35 Ndipo Gaala mwana wa Ebedi anaturuka, naima polowera pa cipata ca mudzi; nauka Abimeleki ndi anthu anali naye m'molalira.
Werengani mutu wathunthu Oweruza 9
Onani Oweruza 9:35 nkhani