Oweruza 9:49 BL92

49 Ndi anthu onse anadulanso yense nthambi yace, natsata Abimeleki, naziika pangaka, natentha nazo ngakayo ndi moto; motero anthu onse a nsanja ya ku Sekemu anafanso, amuna ndi akazi ngati cikwi cimodzi.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:49 nkhani