Oweruza 9:54 BL92

54 Pamenepo anaitana msanga mnyamata wace wosenza zida zace, nanena naye, Solola lupanga lako nundiphe, angamanenere anthu, ndi kuti, Anamupha ndi mkazi. Nampyoza mnyamata wace, nafa iye.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:54 nkhani