Oweruza 9:6 BL92

6 Pamenepo anasonkhana eni ace onse a ku Sekemu, ndi nyumba yonse ya Milo, namuka namlonga Abimeleki ufumu pa thundu wa coimiritsa ciri m'Sekemu.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 9

Onani Oweruza 9:6 nkhani