Cibvumbulutso 12:1 BL92

1 Ndipo cizindikilo cacikuru cinaoneka m'mwamba; mkazi wobvekedwa dzuwa, ndi mwezi ku mapazi ace, ndi pamutu pace korona wa nyenyezi khumi ndi ziwiri;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 12

Onani Cibvumbulutso 12:1 nkhani