Cibvumbulutso 12:4 BL92

4 Ndipo mcira wace uguza limodzi la magawo atatu a nyenyezi zam'mwamba, nuziponya padziko. Ndipo cinjoka cinaimirira pamaso pa mkazi akuti abale, kuti, akabala, ico cikalikwire mwana wace.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 12

Onani Cibvumbulutso 12:4 nkhani