6 Ndipo mkazi anathawira kucipululu, kumene ali nayo mbuto yokonzekeratu ndi Mulungu, kuti kumeneko akamdyetse masiku cikwi cimodzi ndi mazana awiri mphambu makumi asanu ndi limodzi.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 12
Onani Cibvumbulutso 12:6 nkhani