Cibvumbulutso 12:9 BL92

9 Ndipo cinaponyedwa pansi cinjoka cacikuru, njoka yokalambayo, iye wochedwa mdierekezi ndi Satana, wonyenga wa dziko lonse; cinaponyedwa pansi kudziko, ndi angelo ace anaponyedwa naye pamodzi.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 12

Onani Cibvumbulutso 12:9 nkhani