Cibvumbulutso 13:7 BL92

7 Ndipo anacipatsa ico kucita nkhondo ndi oyera mtima, ndi kuwalaka; ndipo anacipatsa ulamuliro wa pa pfuko liri lonse, ndi anthu, ndi manenedwe, ndi mitundu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 13

Onani Cibvumbulutso 13:7 nkhani