Cibvumbulutso 13:8 BL92

8 Ndipo adzacilambira onse akukhala padziko, amene dzina lao silinalembedwa m'buku la moyo la Mwanawankhosa, wophedwa kuyambira makhazikidwe a dziko lapansi,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 13

Onani Cibvumbulutso 13:8 nkhani