Cibvumbulutso 14:8 BL92

8 Ndipo anatsata mngelo wina mnzace ndi kunena, Wagwa, wagwa, Babulo waukuru umene unamwetsako mitundu yonse ku vinyo wa mkwiyo wa cigololo cace.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 14

Onani Cibvumbulutso 14:8 nkhani