7 ndi kunena ndi mau akuru, Opani Mulungu, mpatseni ulemerero; pakuti yafika nthawi ya ciweruziro cace; ndipo mlambireni iye amene analenga m'mwamba ndi mtunda ndi nyanja ndi akasupe amadzi,
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 14
Onani Cibvumbulutso 14:7 nkhani