1 Ndipo ndinamva mau akuru ocokera kuKacisi, akunena kwa angelo asanu ndi awiri, Mukani, ndipo tsanulirani kudziko mbale zisanu ndi ziwiri za mkwiyo wa Mulungu.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 16
Onani Cibvumbulutso 16:1 nkhani