Cibvumbulutso 15:8 BL92

8 Ndipo Kacisi anadzazidwa ndi utsi wocokera ku ulemerero wa Mulungu ndi ku mphamvu yace; ndipo palibe munthu anakhoza kulowa m'Kacisi kufikira ikatha miliri isanu ndi iwiri ya angelo asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 15

Onani Cibvumbulutso 15:8 nkhani