19 Ndipo 2 cimudzi cacikuruco cidagawika patatu, ndi midzi ya amitundu inagwa; ndipo 3 Babulo waukuru unakumbukika pamaso pa Mulungu, kuti aupatse cikho ca vinyo wamkali wa mkwiyo wace.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 16
Onani Cibvumbulutso 16:19 nkhani