17 Pakuti m'ora limodzi casanduka bwinja cuma cacikuru cotere. Ndipo watsigiro ali yense, ndi yense wakupita panyanja pakuti pakuti, ndi amarinyero, ndi onse amene amacita kunyanja, anaima patali,
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18
Onani Cibvumbulutso 18:17 nkhani