16 nadzanena, Tsoka, tsoka, mudzi waukuru wobvala bafuta ndi cibakuwa, ndi mlangali, wodzikometsera ndi golidi, ndi mwala wa mtengo wace, ndi ngale!
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18
Onani Cibvumbulutso 18:16 nkhani