20 Kondwera pa iye, m'mwamba iwe, ndi oyera mtima, ndi atumwi, ndi aneneri inu; cifukwa Mulungu anauweruzira kuweruzidwa kwanu.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18
Onani Cibvumbulutso 18:20 nkhani