Cibvumbulutso 18:21 BL92

21 Ndipo mngelo wolimba ananyamula mwala, ngati mphero yaikuru, naiponya m'nyanja, nanena, Cotero Babulo, mudzi waukuru, udzapasulidwa kolimba, ndipo sudzapezedwanso konse.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18

Onani Cibvumbulutso 18:21 nkhani