Cibvumbulutso 18:4 BL92

4 Ndipo ndinamva mau ena ocokera Kumwamba, nanena, Turukani m'menemo, anthu anga; kuti mungayanjane ndi macimo ace, ndi kuti mungalandireko ya miliri yace;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18

Onani Cibvumbulutso 18:4 nkhani