3 Cifukwa ndi vinyo wa mkwiyo wa cigololo cace mitundu yonse idagwa; ndipo mafumu a dziko anacita naye cigololo; ndipo ocita malonda a dziko analemera ndi mphamvu ya kudyererakwace.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18
Onani Cibvumbulutso 18:3 nkhani