7 Monga momwe unadzicitira ulemu, nudyerera, momwemo muucitire eouzunza ndi couliritsa maliro: pakuti unena mumtima mwace, Ndikhala ine mfumu, wosati wamasiye ine, wosaona maliro konse ine.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18
Onani Cibvumbulutso 18:7 nkhani