8 nadzaturuka kudzasokeretsa amitundu ali mu ngondya zinai za dziko, Gogo, ndi Magogo, kudzawasonkhanitsa acite nkhondo: ciwerengero cao ca iwo amene cikhala ngati mcenga wa kunyanja.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 20
Onani Cibvumbulutso 20:8 nkhani