2 Ndipo ndinaona mzinda woyerawo, Yerusalemu watsopano, ulikutsika Kumwamba kwa Mulungu, wokonzeka ngati mkwatibwi wokometsedwera mwamuna wace.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 21
Onani Cibvumbulutso 21:2 nkhani