Cibvumbulutso 21:3 BL92

3 Ndipo ndinamva mau akuru ocokera ku mpando wacifumu, ndi kunena Taonani, cihema ca Mulungu ciri mwa anthu; ndipo adzakhalitsa nao, ndi iwo adzakhala anthu ace, ndi Mulungu yekha adzakhala nao, Mulungu wao;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 21

Onani Cibvumbulutso 21:3 nkhani