Cibvumbulutso 22:9 BL92

9 Ndipo ananena kwa ine, Tapenya, usacite; ndine kapolo mnzako, ndi mnzao wa abale ako aneneri, ndi wa iwo akusunga mau a buku ili; lambira Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 22

Onani Cibvumbulutso 22:9 nkhani