Cibvumbulutso 3:18 BL92

18 ndikulangiza ugule kwa Ine golidi woyengeka m'moto, kuti ukakhale wacuma, ndi zobvala zoyera, kuti ukadzibveke, ndi kuti manyazi a usiwa wako asaoneke; ndi mankhwala opaka m'maso mwako, kuti ukaone.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 3

Onani Cibvumbulutso 3:18 nkhani