Cibvumbulutso 3:17 BL92

17 Cifukwa unena kuti ine ndine wolemera, ndipo cuma ndiri naco, osasowa kanthu; ndipo sudziwa kuti ndiwe watsoka, ndi wocititsa cifundo, ndi wosauka, ndi wakhungu, ndi wausiwa;

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 3

Onani Cibvumbulutso 3:17 nkhani