Cibvumbulutso 6:1 BL92

1 Ndipo ndinaona pamene Mwanawankhosa anamasula cimodzi ca zizindikilo zisanu ndi ziwiri, ndipo ndinamva cimodzi mwa zamoyo zinai, nicinena, ngati mau a bingu, Idza.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 6

Onani Cibvumbulutso 6:1 nkhani