Cibvumbulutso 6:2 BL92

2 Ndipo ndinapenya, ndipo taonani, kavalo woyera, ndipo womkwerayo anali nao uta; ndipo anampatsa korona; ndipo anaturukira wolakika kuti alakike.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 6

Onani Cibvumbulutso 6:2 nkhani