Cibvumbulutso 6:4 BL92

4 Ndipo anaturuka kavalo wina, wofiira: ndipo anampatsa iye womkwera mphamvu yakucotsa mtendere pa dziko ndi kuti aphane; ndipo anampatsa iye lupanga lalikuru.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 6

Onani Cibvumbulutso 6:4 nkhani