Cibvumbulutso 6:5 BL92

5 Ndipo pamene anamasula cizindikilo cacitatu, ndinamva camoyo cacitatu nicinena, Idza. Ndipo ndinapenya, taonani, kavalo wakuda; ndipo iye womkwera anali nao muyeso m'dzanja lace.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 6

Onani Cibvumbulutso 6:5 nkhani