10 Ndipo liri nayo micira yofanana ndi ya cinkhanira ndi mbola; ndipo m'micira mwao muli mphamvu yao yakuipsa anthu miyezi isanu.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 9
Onani Cibvumbulutso 9:10 nkhani