Cibvumbulutso 9:13 BL92

13 Ndipo mngelo wacisanu ndi cimodzi anaomba, ndipo ndinamva mau ocokera ku nyanga za guwa la nsembe lagolidi liri pamaso pa Mulungu,

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 9

Onani Cibvumbulutso 9:13 nkhani